See more of Malawi News Agency on Facebook

Related Pages
- Organization
- POLITICS & ELECTIONS FORUMPolitical Organization
- Breaking News in MalawiMedia/News Company
- NyasaTimes NewspaperNews & Media Website
- Advertising/Marketing
- Malawi Daily News OnlineNewspaper
- Nation Publications LimitedMedia/News Company
- Media/News Company
- Citizen OnlineMedia/News Company
- Zodiak Broadcasting Station -ZBS TVTV Channel
- MBC Malawi LtdMusic
Recent Post by Page
BREAKING NEWS: EU OBSERVER MISSION IKUZAPEMPHA MUNTHARIKA KUTI ATULU...SE PANSI UDINDO WAKE
European Union observer mission yonse yomwe inalipo nthawi yachisankho yalengeza kuti ibwelanso ku dziko lino mawa kuzakhala pansi ndi mtsogoleri wa dziko lino Peter Muntharika ndinso kumupempha kuti atule pansi udindo wake mwawulemu ngati Court litamupeza kuti iye ndi olakwa.
Malingana ndima report omwe atipeza kuchokela ku EU, bungweli lamvesedwa kuti masankho sanayende bwino ndipo akuyenela kuchitikanso.
Pofuna kulimbikisa ufulu ndi malamulo a dziko lino, bungwe la EU laganiza zokambilana ndi Peter Muntharika kuti atule pansi udindo wake mwaulemu ndinso kuzapempha a Malawi kuti azavomeleze chigamulo cha court See More
TB JOSHUA WATI U VICE PRESIDENT WA CHILIMA SUNATHE (segulani ma pict...ures pa number kuti muone)
TB Joshua anapempha anthu omwe amapemphela nawo mu tchalitchi mwake kuti amuthandize kupemphelela Vice President modzi wakale muno mu Africa ati ponena kuti u Vice President wake sunathe ndinso akumana ndi mikwingwilima pogwila ntchito yake.
Monga mukuonela pa number 6 ndimene TB Joshua walembela pa Facebook page yake.
Ulosiwu ukulunjika kwa Dr Saulos Chilima yemwe ali Vice President wakale mdziko lino ndinso ndiyekhayo yemwe ali ndi mulandu okhuza zisankho muno mu Africa.
Pali unthenga wina waboza omwe Nyasatimes ikufalisa onena kuti TB Joshua wanena kuti "NO CHANGE FOR MALAWI" ife a Malawi News Agency chinatikomela ntima kuyimbila phone mpingo wa TB Joshua kuti tipeze umboni weni weni pa nkhaniyi koma tapeza kuti unthengawu ngwaboza ndipo sukuyenela kumveledwa.
Mukasegula page ya TB Joshua mupeza kuti TB Joshua sananene kalikonse kokhuza Malawi ndinso kuti sanalunjike mwachindunji pa nkhani yokhuza Vice President powopesa zipolowe bwalo lisanagamule.
Joshua sanalunjike nkhani yokhuza vice President ku Malawi kamba amaziwa kuti zitha kuyambisa chipolowe munadela ambili maka pa nthawi ino yomwe asilikari sanakonzeke kuyamba ntchito yokhazikisa bata.
Muunthenga wake TB Joshua wati iye apemphelela Vice President wakale wa dziko lino kamba azakhala ndi pressure yothana ndimavuto mu m'dziko lino pakanthawi kochepa kuti masankho achitike malingana ndima report omwe achokela ku mpingo wa TB Joshua See More
AKULU AKULU A DPP APANGA UPO OFUNA KUPHA MBONI ZA MCP NDI UTM NDICHO...LINGA CHOTI AKAWINE MULANDU KU COURT LA SUPREME
Kagulu ka akuluakulu ena a DPP monga Peter Muntharika, Charles Mchacha, Nicholas Dausi, Grezeeder Jeffrey, Chimunthu Banda, Ntompwa 1, Duncan Mwapasa ndinso bodyguard wa Peter Muntharika Norman Chisale apanga upo oti aphe mboni zikuzikulu za MCP ndi UTM pazolinga zoti akakasuma kubwalo la Supreme mbali zosusa zizalephele kukhala ndi mboni zokwanila.
Izi zaziwika lero pomwe Nicholas Dausi ndi wamkulu wapolisi usiku uno anachitisa msonkhano ndi apolisi ena okwanila 40 ochokela ku mwela komwe mwazina amakambilana zoyamba kupha Daud Suleman kusilizila Ndasauka.
Panthawi ino yomwe antolankhani athu apeza izi, mboni zina za DR Saulosi Chilima zikukumana ndimikwingwilima yochokela kwa apolisi ena omwe akumapita kumanyumba kwawongati mbava, mbonizi ndimonga Miriam Gwalidi ndi Darlington Ndasauka.
Nawo a Daud Suleman omwe ndi mboni ya Dr Lazalous Chakwera akukumana ndi mavuto ochuluka kamba anthu a DPP akumapita ku nyumba kwake usiku ndimifuti.
Pakanali pano apolisi angoti akufufuzabe.
Norman Chisare ndi oophya kwambili ndipo amaziwa kuphedwe kamunthu mwachisilikari ndiyenso anapha Njaunju See More












